Lloyd Aaron anasewera nawo mu masewero omwe timu yake ya Muaither SC inagonjetsa Al-Wab Club 1-0 mu ligi yaing'ono yaku Qatar.
Ichi chinali chipambano chawo choyamba poti mmasewero oyamba analepherana 3-3.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores