NEWS
Chimwemwe Nkhoma akupimidwa ndipo ngati akhonze asaina mgwirizano ku Mighty Mukuru Wanderers.
Iye ndi wotseka kumbuyo ku timu ya Mayamiko Stars komatu ndandanda wa mayina ku Flames amuonetsa kale kuti ndi wa Wanderers.
Iye ali ndi zaka 20.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores