NKHANI
Timu ya Mighty Mukuru Wanderers yachotsa osewera asanu, osewera wa ndi
(1). Miracle Gabeya (out of contract) (2). Chiukepo Msowoya (out of contract) (3). Robin Ngalande (out of contract) (4). Adeleke Kolawole(out of contract) (5). Matthews Masamba ( lack of game time)
Paliso chiyembekezo chakuti timuyi posachedwapa ikhale ikusaina osewera otseka kumbuyo watimu ya Chitipa United, Chris Lwemba kuti akalowe mmalo mwa Gabeya.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores