Timu ya FCB Nyasa Big Bullets idzalowera ku Dowa pa 16 komanso pa 17 March komwe adzakakhale ndi masewero apaubale pa bwalo la Champions.
Timuyi idzasewera ndi Kambelembele FC yaku Mdzaleka ku Dowa komweku pa 16 ndipo mawa lake idzakumana ndi Chatoloma ADMARC yaku Kasungu pa bwaloli.
Mwini wake wa bwaloli, a Msayiwale Kabvina, ndi amene akonza masewerowa.
Mutumizilani pa 0991509953
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores