Wosewera watimu ya Flames Richard Mbulu wabwelera kutimu yake yakale ya MAFCO atakhala zaka akusewera mpira mdziko la South Africa.
Akuluakulu a timu ya MAFCO atsimikiza zankhaniyi.
Izi zikudza pamene panali malipoti oti akuluakulu aku MAFCO anauza wosewerayu kuti abwelere kuno kumudzi kuzapitiliza ntchito ya usirikali.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores