Timu ya Malawi yalephera kuchita bwino kumpikisano wa 2022 Hollywoodbets COSAFA Cup omwe ukuchitikira mdziko la South Africa.
Pa masewero awiri omwe timuyi yasewera ndi matimu a Lesotho komanso Eswatini sinapambane ali onse.
[DELETED]
Pa masewero-wa, Malawi yagonja ndi Lesotho, 2-1 komanso kulepherana ndi Eswatini, 1-1.
Timu ya dziko linoyi yatsala ndi masewero amodzi omwe ikumane ndi Mauritius.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores