Football Association of Malawi (FAM) pamodzi ndi kampani ya Airtel Plc akhazikitsa mpikisano wa Airtel Top 8 mawa mu mzinda wa Blantyre.
Mtsogoleri wa bungwe la FAM Walter Nyamilandu watsimikiza za nkhaniyi.
Malingana ndi a Nyamilandu mpikisanowu aukhazikitsa ndi masewero apakati pa Nyasa Big Bullets ndi MAFCO omwe achitikire pa bwalo la Kamuzu ku Blantyre.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores