Timu ya Nyasa Big Bullets yati yakonzeka kugonjetsa Amazulu m'masewero achibwerenza a mpikisano wa CAF ndi Amazulu lero.
Mphunzitsi wa timuyi, Callisto Pasuwa wati osewera onse alipo ndipo ali ndi chikhulupiliro kuti achita bwino.
BB 0-2Amazulu
Maule zabwno zonse lero
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores