Unduna wa zaumoyo walengeza kuti anthu tsopano akhoza kuyamba kuonera masewero a mipikisano yosiyanasiyana kutsatira kutsikwa kwa chiwerengero cha anthu omwe akudwala matenda a Covid-19.
Nduna ya zaumoyo Khumbize Kandodo Chiponda ndiyo yalengeza izi.
A Chiponda ati theka la chiwerengero chomwe amalowa masewero ndiwo aziwalola.
Apa anduna akhoza makapomwe week yamawa tilini game ya amazulu tikuthokozapamenepa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores