Bwanji ma predictions anga akuchepa m'malo mwa 27 ikuwonesa 8 predictions zikukhala bwanj admin
Oky boss ndakumvani
Team ya might tigers ikufuna anthu akufuna kwabwno kuti ayithandze ku nkhani ya ndalama potengeraso kuti ndi team yaikulu,yolimbikira
Game ya dzuro sindikumvesa kuti zinatha bwanj, mpira unaseweredwa kma?
Anasewera koma palibe yemwe anagoletsa. Wathera 0-0.
Prediction 1-1 prediction
Prediction 0-1 prediction💯
Prediction 3-0 prediction
Prediction 0-2 prediction