Timu ya Mighty Wanderers yati ikufuna kugulitsa katundu wake wina pofuna kupeza ndalama zoyendetsera ntchito zake komanso kulipira osewera.
Izi ndi malingana ndi wapampando wa timuyi, Simon Sikwese.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores