Victor Limbani wachoka ku timu ya Silver Strikers kutsatira kutha kwa kontrakiti yake pa 31 August, 2020.
Mkulu woyendetsa zintchito za timuyi, Thoko Chimbali, wati wosewerayu anali wapamwamba.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores