Wosewera wa timu ya Flames, Gabadinho Mhango, wakhala katswiri wosewera bwino kuposa anzake onse mu mwezi wa January ku South Africa.

Mhango ndi yemwenso akutsogola ndi zigoli mu ligi ya m'dziko-lo.

13 Feb 15:16

Share on Facebook
Post Predictions & Updates

Login with Facebook to post predictions, updates & live scores