Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Mphunzitsi wa timu ya anyamata osaposa zaka 17, Deklerk Msakakuona, wasankha mphunzitsi wogwirizira ku Kamuzu Barracks, Ted Kalinda, ngati womuthandizira mpikisano wa COSAFA usanayambe mwezi uno. times.mw
Malawi to host 2022 Cosafa - The Times Group Malawi Council for Southern Africa Football Association (Cosafa) says Malawi will host the Under-17 zonal qualifiers in December, 2022. The competition... times.mw
Bungwe la COSAFA latsimikiza kuti dziko lino lichititse mpikisano wa wosewera mpira wa miyendo koma osapyola za 17 chaka chino.
Izi zatsimikizidwa pa mkumano omwe mamembala a bungweli anali nawo.
Malawi 1 - 0 Zambia
Malawi to host COSAFA Senior Tournament and U-17 next year.
COSAFA President revealed this during the prize presentations.
He attributes the development following the support rendered by Malawians.
COSAFA U-17 Youth Championship Awards Best Fair Play Team - Eswatini Best Goalkeeper - David Minganja (Zambia) Top Goal Scorers - Simon Cipriano, Nickson Ng'ambi, Valdemiro Domingos (5 goals)
Player of the tournament - Moses Mulenga (Zambia)
Standings at COSAFA U-17 Youth Championship.
1. Zambia
2. Mozambique
3. Angola
4. Eswatini
Zambia are the champions of 2019 COSAFA U-17 Championship after beating Mozambique 2 nil in the final game.
During the tournament Zambia has not lost a game.
Defending champions of COSAFA U-17, Angola have finished on position 3 after beating Eswatini 5 nil.
Angola will receive bronze medal.
A
Local sports journalists have been asked to embrace new ways of reporting as one way of enhancing their skills.
SABC Senior Sports Reporter, Velile Mnyandu, made the appeal on Friday in Blantyre.
Timu ya Angola yomwe imasunga ukatswiri wa mpikisano wa COSAFA U-17 yatuluka itagonja 2-0 ndi Zambia.
M'masewero-wa m'chigawo choyamba mbali zonse zinalephera kupeza zigoli.
Defending Champions of COSAFA Youth Tournament, Angola are out after suffering a 2 nil defeat against Zambia.
Zambia will battle it out with Mozambique in the final game of the competition.
Mozambique are through to the finals of COSAFA Youth Championship as they await the winner between Angola and Zambia.
Mphunzitsi wa timu ya chisodzera ya dziko lino, Deklerk Msakakuona, wapepesa ati kamba kotuluka mu mpikisano wa COSAFA omwe uli mkati ku Blantyre.
Ndime ya semifinals ya COSAFA ikuyembekezeka kuseweredwa Lachisanu likudza-li.
Zambia, Eswatini, Angola ndi Mozambique.
Timu ya Malawi yatuluka mu mpikisano wa COSAFA U-17 kutsatira kugonja ndi timu ya Zambia 3-2.
Malawi imayenera kuti ipambane pofuna kufika mu ndime ina ya mpikisano-wu.
Zambia ndi Eswatini apitilira.
Mphunzitsi wa timu ya chisodzera ya dziko lino, Deklerk Msakakuona, wati timuyi yakonzeka kuchita bwino pa masewero awo lero ndi Zambia.
Msakakuona wati achita chili chonse kuti achite bwino.
Matimu a Angola ndi Mozambique afika mu ndime ya matimu 4, semifinals m'chingerezi mu mpikisano wa COSAFA.
Matimu-wa afika mu ndimeyi ndi mapoint 7 aliyense.
Ndipo Comoros ndi Lesotho atuluka.
Mphunzitsi wa timu ya dziko lino ya chisodzera, Declerck Msakakuona, wati achita chili chonse chotheka kuti apambane masewero awo ndi Eswatini.
Organizing committee for COSAFA U-17 tournament has introduced a fee to the Junior Flames games as a security measure and to control the crowd.
Spectators will by the tickets in all designated places set by FAM.