Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Timu ya Angola yomwe imasunga ukatswiri wa mpikisano wa COSAFA U-17 yatuluka itagonja 2-0 ndi Zambia.
M'masewero-wa m'chigawo choyamba mbali zonse zinalephera kupeza zigoli.
Defending Champions of COSAFA Youth Tournament, Angola are out after suffering a 2 nil defeat against Zambia.
Zambia will battle it out with Mozambique in the final game of the competition.
Mozambique are through to the finals of COSAFA Youth Championship as they await the winner between Angola and Zambia.
Mphunzitsi wa timu ya chisodzera ya dziko lino, Deklerk Msakakuona, wapepesa ati kamba kotuluka mu mpikisano wa COSAFA omwe uli mkati ku Blantyre.
Ndime ya semifinals ya COSAFA ikuyembekezeka kuseweredwa Lachisanu likudza-li.
Zambia, Eswatini, Angola ndi Mozambique.
Timu ya Malawi yatuluka mu mpikisano wa COSAFA U-17 kutsatira kugonja ndi timu ya Zambia 3-2.
Malawi imayenera kuti ipambane pofuna kufika mu ndime ina ya mpikisano-wu.
Zambia ndi Eswatini apitilira.
Mphunzitsi wa timu ya chisodzera ya dziko lino, Deklerk Msakakuona, wati timuyi yakonzeka kuchita bwino pa masewero awo lero ndi Zambia.
Msakakuona wati achita chili chonse kuti achite bwino.
Matimu a Angola ndi Mozambique afika mu ndime ya matimu 4, semifinals m'chingerezi mu mpikisano wa COSAFA.
Matimu-wa afika mu ndimeyi ndi mapoint 7 aliyense.
Ndipo Comoros ndi Lesotho atuluka.
Mphunzitsi wa timu ya dziko lino ya chisodzera, Declerck Msakakuona, wati achita chili chonse chotheka kuti apambane masewero awo ndi Eswatini.
Organizing committee for COSAFA U-17 tournament has introduced a fee to the Junior Flames games as a security measure and to control the crowd.
Spectators will by the tickets in all designated places set by FAM.