Ngakhale tikutumiza ma numbers sizikuyenda pano pa owinna.com chonde chonde admin tithandizeni tiuzeni zoona kuti tiyendele zimodzi ngati tidzalandile mphoto zathu.
Tayamba kupereka mphoto zanu. Amene anawina Sabata yothera 26 July alandira mphoto zawo. Ena azilandira masiku akubwera wa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores