Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Mageme alibwanj
#TNMSuperLeague LIVE: Karonga Utd 0-1 Mukuru Wanderers KB 0-1 Silver Strikers Dedza Dynamos 0 - 1 Civil Service Tigers 0-1 Ekwendeni Hammers
1 _0
Wanders Ilitha bwa
MULIBWANJI
XTA AOND
Links
@joseph
KWABWERA OwinnaโกLite! Ngati mumafuna kutsatira zampira mwachangu, ngakhale data ili yochepa kapena netiweki ikuvuta, yankho lafika ndi OwinnaโกLite.
OwinnaโกLite, ikuthandizani kutsata magemu, ma log table ndi nkhani ndi kulosera: - mwachangu โก - mosunga data ๐ - ngakhale muli kovuta netiweki ๐
Pitani pa Owinna.com/lite
Messi leaves PSG
Christophe Galtier has just confirmed that Leo Messi will leave Paris Saint-Germain ๐ด๐ต๐ฆ๐ท
โI had a privilege of coaching the best player in the history of football โ this weekend it will be Messiโs last match at PSG at the Parc des Princes against Clermontโ, PSG coach says.
Sevilla beat Roma 4-1 on penalties after a 1-1 draw to win their seventh UEFA Europa League title.
Wosewera wa FCB Nyasa Big Bullets, Hassan Kajoke tsopano ndimfulu poti wabweza ndalama yokwana MK3.9 million.
Bungwe la FAM linalamula katswiriyu kuti abweze ndalamazi atalepherana ndi Silver Strikers pankhani za mgwirizano.
FAM linamupatsa Kajoke masiku asanu kuti ngati satero, sadzaseweranso mpira mdziko muno ndi kunja.
Tsamba la Wa Ganyu latsimikiza kuti Kajoke wabweza ndalamayi komanso MK 200, 000 ngati chindapusa ku bungwe la FAM.
Pano wosewerayi ndi mfulu kusewera mpira tsopano.
Katswiri wa FCB Nyasa Big Bullets,Hassan Kajoke sanapelekebe ndalama zomwe anauzidwa kuti kuti atero ndi bungwe la FAM pasanathe masiku asanu.
Kajoke anauzidwa kuti abweze ndalama zokwana K3.9million zomwe anasayina ngati mgwirizano ndi Silver Strikers chifukwa ndondomeko zambiri zinaphwanyidwa.
Kulephera kupeleka masikuwa atadusa Kajoke azalesedwa kusewera mpira mdziko muno komanso kunja, FAM inatero.
Pofika lero Silver Strikers kudzera mwa mlembi wa board a Peter Masiye ati timuyi yatumiza ndalama zokwana K900, 000 zomwe anauzidwa ngati chindapusa.
Choncho Silver Strikers yapempha FAM kuti liletse Kajoke kuti asiye kusewera mpira chifukwa sanakwanilise zomwe anauzidwa kuchita.
Mauricio Pochettino has decided that Joรฃo Fรฉlix will not play at Chelsea next season, Atlรฉtico Madrid president Enrique Cerezo has confirmed โ
๐ฃ๏ธ โWe have been informed that Poch does not count with Joรฃo Fรฉlix for Chelsea. He will return here, weโll seeโฆ weโve nothing planned."
Malipoti mdziko la France akuonetsa kuti timu ya mpira wa miyendo ya atsikana ya PSG ikufuna zintchito za Tabitha Chawinga yemwe akusewera ku Inter Milan.
Chawinga wamaliza patsogolo mundandanda wa atsikana omwetsa zigoli ku Seria A pamene wamaliza ndi zigoli 23. Iyeyi wakhalanso mtsikana oyamba muno mu Africa kupanga izi ku Italy.
Source: Le Parisien
Chelsea has announced Mauricio Pochettino as the clubโs new head coach!
Mauricio Pochettino has signed a two-year contract with Chelsea, with a club option for a further year.
New