Malipoti mdziko la France akuonetsa kuti timu ya mpira wa miyendo ya atsikana ya PSG ikufuna zintchito za Tabitha Chawinga yemwe akusewera ku Inter Milan.
Chawinga wamaliza patsogolo mundandanda wa atsikana omwetsa zigoli ku Seria A pamene wamaliza ndi zigoli 23. Iyeyi wakhalanso mtsikana oyamba muno mu Africa kupanga izi ku Italy.
Source: Le Parisien
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores