Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
0999955229
For WhatsApp group?
Blue Engle
mwasewelo atha bwanj
Tayika mmene athera.
Flames head coach, Meke Mwase says his charges are geared up for today's game against Eswatini.
Mwase says the boys know the importance of winning the game with a good margin.
TN Stars squad travelling to North: Fia, China Chirwa, Viyuyi, Davie; Chipolopolo, L.Banda, Chizuzu, Siwu, Maliwata, Mthini, Pipe; Jumo, Joseph, Dinga, Msewa, Phiri, T.Banda, Jekapu, Pashane, Kotei.
Note that Nyasa Big Bullets, BE FORWARD Wanderers and Silver Strikers will not play TNM Super League matches this week.
This follows their contribution of players to Malawi National Football Team, Flames.
Flames have safely arrived in Eswatini some hours ago ahead of a match against the country's national football team.
At 3:00 PM CAT, the team is expected to train at the venue of the game.
Osewera kutsogolo kwa Nyasa Big Bullets, Collen Nkhulambe, asewelera timu ya Mzuni kwa chaka chimodzi pa ngongole.
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino, Flames lero inyamuka mdziko muno pomwe ikupita kukasewera ndi Eswatini Loweluka likudza-li.
Mphunzitsi wa timuyi watenga osewera makumi awiri (20).
Matimu a Silver Strikers komanso Nyasa Big Bullets ati aonetsetsa kuti alembetsa nawo pa matimu omwe atenge nawo mbali mu mpikisano wa CAF Champions ndi Confederation chaka chino.
tipatsileni
FLAMES SQUAD: Kakhobwe, Munthali; Dennis, Sanudi, Cholopi, Petro, Lanjesi, G. Chirwa, Kalema; Manyozo, Phiri, Mkwate, Idana, Mhone, C. Chirwa; Simkonda, Mkanda, Msowoya, Kajoke & Muyaba.
Mphunzitsi wa timu ya Flames, Meke Mwase watulutsa ndandanda wa osewera omwe akuyembekezeka kukasewera ndi Eswatini Loweluka likudza-li.
Mphunzitsi wa timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino, Meke Mwase lero akuyembekezeka kutulutsa ndandanda wa osewera omwe akasewere ndi Eswatini Loweluka likudza-li.
Ligi ya m'chigawo cha pakati ya Chipiku iyamba Loweluka likudza-li.
Malingana ndi chikalata chomwe Owinna yaona pano matimu omwe akufuna kutenga nawo mbali akuyenera kulembetsa.
Bwalo la Chiwembe lalephera kuyamba kugwira ntchito kumathero a mwezi wa March pomwe zinthu zina zinali zisanathe pa bwalo-li. Bwalo la Chiwembe ikuyembekezeka kuyamba kugwira ntchito posachedwapa.
Timu ya Flames yati zokonzekera zake zikuyenda bwino patsogolo pa masewero awo ndi Eswatini Loweluka.
Dzulo osewera ali Ku timuyi ayambiranso kuchita zokonzekera kuchokera ku ma club awo.