Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
premier bet
uchizi bado
Thumbsup palibetso pa malawi pano chakumwa chozuna kwambiri
Nyasa big bullets vs beforward
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino, Flames, yayamba kuchita zokonzekera zake patsogolo pa masewero ake ndi Eswatini pa 14 May.
Timuyi ikuchita zokonzekera-zi mu mzinda wa Blantyre ku Chiwembe.
Otsatira timu ya BE FORWARD Wanderers ati aphunzitsi a timuyi atule pansi udindo wawo ponena kuti alephera ntchito.
Wapampando wa masapota ku timuyi, Melvin Kunika wanena izi kutsatira kugonja dzulo.
2
Pa 14 may, Silver ikudzayambira pamene yamalizirapa, choncho, iwe Tunde ndi nzako wa Mkandayo samalani
Thanks guys
Ikutha bwanji game noma ndi silver?
Akudzulidwa anyamata a Noma
Be forward wanders 1 Silver strickers 2
Dr John Paul wathandiza timu ya Mchinji Boma Stars poiperekera K200,000 yolowera mu season ya 2019/20 ya Chipiku.
Izi zadza pomwe timuyi imasowa thandizo kuti ilipire ndalama yolowera mpikisano-wu.
Zonse zokonzekera zokhudza kuyamba kwa masewero amu ligi ya Chipiku zatha ndipo lero mpikisano-wu autsegulira.
Izi ndi malingana ndi mmodzi waakulu oyendetsa mpikisano-wu, Antonio Manda.
Zokonzekera zonse zokhudza mpikisano wa Airtel Top 8 zatha pomwe lero masewero mu mpikisano-wu akuyamba.
Dzulo matimu alandira zovala zomwe agwiritse ntchito pa masewero awo mu mpikisano-wu.
gitafe vs maridir
karonga 2 moyal 1
Karonga United ilibe gemu week end ino.
Bonanza yomwe yinati yichitike week yino ku Mchinji yalepheleka kamba ka ntchito zina zomwe othandiza bonanzayi ali nazo ku Lilongwe.
Silver Strikers Squad to play against Wanderers; Munthali, Thom, Micheta, Wayekha, Mpachika, Mwendepeka, Kalema, Robert, Fodya, Wali, Shelif, Limbani, Maganizo, Nyemera, Nyoni, Paipi, Mwaira, Chimodzi.
Shamama, Pangani, Muyaba, Tetteh, Philemon.
Timu ya Silver Strikers yafika mu mzinda wa Blantyre pomwe asewere ndi Wanderers mu Airtel Top 8 m'masewero oyamba.
Yemwe amayang'anira timu ya Ntopwa, Isaac Jomo Osman, wati ngakhale sanachite bwino masewero awo oyambira mu ligi, ali chikhulupiliro kuti achita bwino masewero otsatira.
Timu ya Wanderers yasaina osewera waku Nigeria, Raphael Udah.
Udah amasewera pakati ngati othandizira kuteteza kumbuyo.
Chaka chino tnm super league ivuta kwambiri aliyese akufuna kukhala pa top
Bungwe loyendetsa masewero a mpira pa dziko lonse la FIFA, laletsa Hellings Mwakasungula kutenga nawo mbali pa zochitika za mpira pomwe amupeza kuti anagulitsa masewero a Flames m'chaka cha 2010.
Pali chikulirano chachikulu pa otsatira timu ya Wanderers komanso Mabankers pomwe aliyense akuti timu yake iwina mu masewero amu Airtel Top 8.
Loweluka likudza-li Wanderers izasewera ndi Silver Strikers.
Timu ya BE FORWARD Wanderers yati season ya 2019/20 ikhala ndi osewera 28 omwe atumikire timuyi.
Akuluakulu oyendetsa mpikisano wa Chitipa District Council Under 17 lero akumana pofuna kuunika momwe mpikisano-wu wayendera.
Akuluakulu ama timu omwe amasewera mu ligi-yi akuitanidwa pa mkumano-wu.
Lifting phiri
Koma anyamata a team ya Flames anakayesetsa
NOMA B CARE, ITS OUR TIME TO REVENGE za fisd cup zimatiwawabe Mabanker moto kuti buuuuuuuuuuuuuuuu!!!!!
Sulom mwayambapo ma fixture anu opoila aja Dwangwa ikukwanisa ma game 4 pomwe ena ali ndi awili. Sulom siizatheka, timaona ngati mwabweranutu muikwanitsa
Mabanker ndi dhilu
Bungwe loyendetsa masewero m'chigawo cha pakati la Central Region Football Association (CRFA) lati mpikisano wa Chipiku uyamba Loweluka likudza-li.
0885258969
Malawi National Football Team, Flames have arrived yesterday, Sunday in the country from Eswatini.
Flames played against Eswatini in 2020 Chan matches a game which ended in a goalless draw.