Sambani wayithyola!
Timu ya Ekhaya FC yatsimikiza kuti mwambo womwe anakonza kuti awonetse osewera watsopano, Precious Sambani, wakanika.
Katswiriyu amayenera kufika ku mwambowu nthawi ya 8 koloko komatu iye sanapezeke mpaka nthawi.
Malipoti otsimikizika akuonetsa kuti Sambani tsopano akupita ku Silver Strikers komwe akalowe mwa Mark Fodya yemwe walowera mdziko la Zimbabwe.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores