NKHANI
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yalengeza kuti katswiri wawo wapakati, Frank Willard wavulala.
Timuyi yalengeza za nkhaniyi kudzera pa tsamba lawo la Facebook ndipo yati iye wavulala lachinayi pomwe anali kupanga nawo zokonzekera patsogolo pa chaka cha mpira cha 2025.
Iwo ati Willard wavulala phazi ndipo sapezeka kwa masabata anayi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores