Bungwe la SULOM lalengeza kuti masewero a Silver Strikers ndi Mighty Tigers omwe amayeneleka kukhala loweruka pa 13 May alepheleka.
Izi zili chonchi chifukwa bwalo la Bingu National Stadium izakhala ndizochitika pokonzekera tsiku la Kamuzu pa 14 May. Choncho masewerowa ayikidwa tsiku lina lomwe sananene.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores