Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Zokonzekera zonse zokhudza mpikisano wa Airtel Top 8 zatha pomwe lero masewero mu mpikisano-wu akuyamba.
Dzulo matimu alandira zovala zomwe agwiritse ntchito pa masewero awo mu mpikisano-wu.
Silver Strikers Squad to play against Wanderers; Munthali, Thom, Micheta, Wayekha, Mpachika, Mwendepeka, Kalema, Robert, Fodya, Wali, Shelif, Limbani, Maganizo, Nyemera, Nyoni, Paipi, Mwaira, Chimodzi.
Shamama, Pangani, Muyaba, Tetteh, Philemon.
Timu ya Silver Strikers yafika mu mzinda wa Blantyre pomwe asewere ndi Wanderers mu Airtel Top 8 m'masewero oyamba.
Pali chikulirano chachikulu pa otsatira timu ya Wanderers komanso Mabankers pomwe aliyense akuti timu yake iwina mu masewero amu Airtel Top 8.
Loweluka likudza-li Wanderers izasewera ndi Silver Strikers.
Former Nyasa Big Bullets midfielder, Raquib Lulu Milanzi, has been unveiled as Airtel Top 8 brand ambassador.
Milanzi also played for Civil Sporting, Nairobi City Stars, Tuska and Caps United.
Officials from Silver Strikers say their game against BE FORWARD Wanderers in Airtel Top 8 will be pay back time. The officials say they want to revenge the FISD Challenge Cup Finals defeat.
Airtel Top 8 is scheduled to commence in April after a successful draw yesterday at Mpira Village, Chiwembe in Blantyre.
FAM is today expected to release fixed dates for first leg games.
Airtel Top 8 draw
Silver Strikers vs BE FORWARD Wanderers,
TN Stars vs Karonga United,
Mzuni vs Civil Sporting,
Kamuzu Barracks vs Masters Security.
Umenewo nde osayamba
Lero matimu omwe asewere mu mpikisano wa Airtel Top 8 adziwa mmene masewero awo oyamba akhalire.
2019 Airtel Top 8 draw will take place on Thursday from 10 am at Mpira Village in Blantyre.
Football Association of Malawi (FAM) officials have confirmed the development.