Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Godfrey Nkakananga ndiye aimbire masewero omaliza amu ndime ya Airtel Top 8 ku Lilongwe.
Nkakananga athandizidwa ndi Clement Kamwendo, Samuel Fudzulani, Alfred Kaphamtengo ndi YZ Chilinda.
Akuluakulu a kampani ya Airtel ati ndi okhutira ndi momwe mpikisano wa Airtel Top 8 wayendera chaka chino.
Frank Magombo wanena izi poyankhula ndi Owinna.
Katswiri oimba nyimbo mdziko muno, Skeffa Chimoto, lero akhala akuimba ku masewero omaliza a mpikisano wa Airtel Top 8.
Katswiriyu akhala akuimba nyimbo zake zosiyanasiyana pa masewero-wa.
Timu ya Karonga United yauuza otsatira timuyi kuti chikho cha Airtel Top 8 chifika kumpoto Lamulungu likudza-li.
Wapampando wa timuyi, Alufeyo Banda, wati zokonzekera za timuyi zikuyenda bwino.
Goal-drought undermines Airtel Top 8 Wakaa! Theme - The Nation Online Though launched under the theme Wakaa! in anticipation of massive goals, the 2019 Airtel Top 8 has produced just 11 goals. No... mwnation.com
Ndime yomaliza ya mpikisano wa Airtel Top 8 ikachitikira mu mzinda wa Lilongwe pa bwalo la Bingu.
Izi ndi malingana ndi zomwe bungwe la FAM lanena.
Silver Strikers idzasewera ndi Karonga United.
Katswiri pa nkhani za masewero mdziko muno, Humphreys Mvula, wati oyendetsa mpikisano wa Airtel Top 8 akuyenera kuika zinthu za pa mwamba zomwe zikachitike ku masewero omaliza pofuna kukopa anthu.
Silver Strikers will play against Karonga United in Airtel Top 8 Finals after beating Masters Security on Sunday.
The match will be played on 29 June, at a venue to be announced by FAM this week.
results
B4ward wanderers 4 :1 Kmuzu baracks
Ndime ya matimu anayi mu mpikisano wa Airtel Top 8 ikhalapo kumapeto kwa sabata ino.
Mpikisano-wu ukuyembekezeka kufika kumapeto kumathero kwa mwezi uno.