Timu ya Chitipa United yasaina katswiri wakale wa Bangwe All Stars ndi Silver Strikers, Friday Osagie, yemwe kwawo ndi ku Nigeria.
Iye wasaina mgwirizano wa zaka ziwiri pomwe wapitako mwa ulere kutsatira kutha kwa mgwirizano wake ndi Goshen City Dedza Dynamos.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores