NKHANI
Bungwe loyendetsa mpira kummwera kwa dziko lino ya Southern Region Football Association yalowa mu mgwirizano ndi kampani ya FINCA Malawi kuti izithandiza ligi yawo yaikulu.
Mwambo wosainirana mgwirizanowu unachitikira ku Chiwembe ku nyumba ya Mpira kummawa kwa lachinayi.
Mu mgwirizanowu, kampaniyi ikhuthula ndalama zokwana K100 million zopita ku ligiyi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores