Ahamad Kung'unde atumikira timu ya FCB Nyasa Big Bullets mu ligi ya chaka cha 2026-27 pomwe wavomera kuti asaina mgwirizano wa zaka ziwiri ndi timuyi.
Mgwirizano wake ndi Mighty Wanderers unatha kale mu September chaka chatha.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores