Timu ya Chilobwe United yatsimikiza kuti Mphunzitsi wawo, Trevor Kajawa, wachoka kutimuyi.
Kajawa akuoneka kuti akufunidwa ndi matimu a Mighty Tigers komanso Songwe Border United kuti mwina awapulumutse asatuluke mu ligi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores