Timu ya Karonga United yatsimikiza kuti katswiri wawo womwetsa zigoli, Allen Chihana, sapezeka kwa ma sabata asanu ndi imodzi (6) kamba koti ndi wovulala.
Timuyi yatsimikiza za izi kudzera pa tsamba lake la mchezo la Facebook kuti katswiriyu wavulala ku zokonzekera za timuyi ndipo madotolo amuuza kuti apume kaye kwa sabata zimenezi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores