Bungwe la Super League of Malawi layika mitengo ya masewero omwe idziyikidwa pa matimu osiyana siyana mu 2024.
Matimu a FCB Nyasa Big Bullets, Mighty Mukuru Wanderers komanso Silver Strikers masewero awo azikhala pa K4,000 pomwe matimu a Chitipa United, Karonga United, MAFCO, Kamuzu Barracks, Bangwe All Stars komanso Dedza Dynamos azipereka K3,000 ndipo otsalawo ndi K2,000.
Bungweli lachita izi kuti lithandize kupeza ndalama zochuluka za pazipata za pa masewero.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores