Banki ya First Capital yalengeza kuti ithandiza mpikitsano wa Four Nations ndindalama zokwana K50 million.
Mpikitsanowu uyamba mwezi uno pa 21 mpaka 26 March 2024 pabwalo la Bingu mudzinda wa Lilongwe.
Maiko a Malawi, Kenya, Zimbabwe, Zambia ndiomwe akhale akutenga nawo mbali mumpikisanowu.
First Capital Bank imathandizanso league ya osewera osapyola zaka 20 komanso imathandiza timu ya Nyasa Big Bullets.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores