LOCAL TRANSFER - Tonny Mbulu to Ekhaya FC
Osewera yemwe anatumikirapo matimu a Mighty Tigers komanso MAFCO FC, Tonny Mbulu wamvana ndi timu ya Ekhaya FC ndipo mgwirizano wachitika mphangalayi season ya 2024 atumikire timuyi muligi ya SRFA ThumbsUp Premier Division League.
Source: Frank Mojah Dzuwa
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores