Umu ndi mmene bwalo la Zomba likuonekera.
Bwaloli linayikidwa kuti litsegulidwa pakati pa miyezi ya September ndi October 2023 kutsatira kuyendera kwa a Fleetwood Haiya ali mtsogoleri wa Super League of Malawi.
Padakali pano tikudikira tsiku lomwe atalengeze kuti ntchito zonse zatha komanso lotsegulira bwaloli.
📸 Laero Lajab
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores