ZIKUYENDA KU FLAMES
Timu ya dziko lino ya Flames yatsika pa ndandanda wa matimu onse padziko lino lonse lapansi pomwe yasuntha ndi phazi limodzi.
Malingana ndi ndandanda omwe bungwe la FIFA latulutsa, timuyi yachoka pa nambala 123 kufika pa 122 mu mwezi uno wa February.
Ngakhale izi zili chomwechi, Flames simasewereko masewero aliwonse mu January pomwe amaonera kaye AFCON.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores