Timu ya Civo United yatenga katswiri wawo wakale, Frank Banda, kuti atumikire timuyi mu chigawo chachiwiri cha ligi ya TNM.
Banda wakhala alibe timu pomwe anamuchotsa ku timu ya Silver Strikers kumayambiliro a chaka chino ndipo wabwereranso kutimu yomwe anachita mu 2012.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores