MBEWE WAPITA KU KARONGA PA NGONGOLE
Timu ya Chitipa United yalengeza kuti katswiri wawo wapakati, Nanson Mbewe, wapita pangongole kutimu ya Karonga United mpaka kumapeto kwa ligi ya chaka chino.
Timuyi yatsimikiza nkhaniyi pa tsamba lawo la mchezo pomwe yati katswiriyu akhala kutimuyo kwa miyezi isanu yokha basi.
Timuyi yamufunira zabwino katswiriyu ndipo wati akachita ntchito yake awapeza kutimuyi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores