Yes. ineyo ndimwa m'modzi amene anachita mwayi kwa olosera a sabata ya Mon, 20-26 Sun, July. Ndikudabwa kuti m'paka lero sindikulandilabe mphoto yanga. Ndikumadzifusa kuti koma ndidzalandila? Nanga ndidzalandila liti?. Ndiuzeni chilungamo admin.
Ineso m'paka lero. Koma sakutiuza zoona admin kuti tidziwe.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores