Masapota a timu ya Mighty Wanderers Lachitatu anapereka ndalama yokwana K100, 000 kwa osewera a timuyi ngati njira imodzi yowathokoza kutsatira kuchita bwino kwawo m'masewero a m'chigawo chakumpoto.
Masapotawa anapereka zokumwa kuphatikizapo madzi kuti zithandizire zokonzekera zawo.
Sabata ino Noma isewera ndi timu ya Red Lions.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores