Osewera ena a timu ya Wanderers akufuna kuthamangitsidwa nyumba zomwe akukhala kaamba kosalipira ndalama ya rent.
Izi ndi malingana ndi zomwe akuluakulu ena a timuyi auza Owinna.
📷 Ark Tembo
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores