Timu ya Nyasa Big Bullets akuidzudzula kaamba kotchingira osewera a timuyi kukasewera matimu ena akunja.
Izi zikudza pomwe timu ya Bullets ikukana kuti sinalandire kalata yokhudza wosewera wawo Banda
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores