Wanderers yachenjeza oimbira mpira mdziko muno kuti asiye kuida timuyi monga akhala akuchitira mbuyo komanso kukondera timu zina.
Mlembi wa masapota a timuyi, Samuel Mponda, ndiye wanena izi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores