Mwini wake wa Ntopwa, Isaac Jomo Osman wati bungwe la FAM likulephera kupititsa patsogolo masewero a mpira mdziko muno pomwe ati amaika chidwi chawo ku ndalama.

11 Mar 21:19

Share on Facebook
Post Predictions & Updates

Login with Facebook to post predictions, updates & live scores