Chikoti Chirwa wachenjeza osewera anzake kuti alewe kukopeka ndi zokamba za yemwe amati ndi m'khalapakati wa osewera ndi matimu, Prince Jere ponena kuti mkuluyu ndi wabodza.

11 Feb 08:22

Share on Facebook
Post Predictions & Updates

Login with Facebook to post predictions, updates & live scores