Timu ya Silver Strikers yati ionjezera wosewera ena omwe atumikire timuyi chaka chino.
Mlembi wa timuyi, Innocent Kadamanja, wanena izi kutsatira kuchoka kwa Khuda Muyaba kupita ku South Africa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores