Yes. ineyo ndimwa m'modzi amene anachita mwayi kwa olosera a sabata ya Mon, 20-26 Sun, July. Ndikudabwa kuti m'paka lero sindikulandilabe mphoto yanga. Ndikumadzifusa kuti koma ndidzalandila? Nanga ndidzalandila liti?. Ndiuzeni chilungamo admin.
Ndi zoona ndipo tikukumvetsetsani, koma tikutsimikiza kuti nonse mulandira mphoto zanu ndithu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores