Pamene olosera bwino kuposa anzawo sabata ya Mon, 10-16 Sun Aug. Akuyembekezela kutumiza ma account number awo. Titsikimizile pano kuti kuchokela sabata ya man, 20-26 Sun July., Man, 27-july---Sun, 2-Aug., Mon, 3-9 Sun, Aug. Sanalandilebe mphoto ya ndalama zawo m'paka lero. NDIYE ADMIN MUTIUZE ZOONA KUTI KUPELEKA MPHOTO KULIPO KAPENA MUNASIYA KUPELEKA M'PHOTOZI? Mutiuze zoona kuti tidzilosera tikudziwa chilungamo chifukwa zutidabwitsano.
Pepani sitinatumizebe mphoto za ndalama kwa omwe anawina kuyambira Sabata yothera 26 July. Tikutsimikiza kuti nonse mulandira mphoto zanu masiku akubwerawa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores