Tikozetse kuti amene sanalandibe mphoto zawo ndi asabata yothera sun, 26-July ndi sun, 2-Aug. Tangoganizani tikukamba za July m'paka lero 7-aug. Zilibwino choncho?
Zoona, sitinatumise mphoto zanu sabata yatha ndi sabata ino, koma tikukonza kuti muzilandira sabata iliyonse ngati kale.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores