update table
Admin moni, ifeyo mongo opanga masewelo amulosela pano pa owinna.com sitili okodwa malingana ndikapelekedwe kamphoto yandalama yomwe olosera bwino kuposa anzawo akumatsidwira. Zikumatenga sabata ziwiri mwinaso ndimasiku wena zomwe zikwiyitsa olosera pano pa owinna.com tikunena pano a sabata yothela 2- Aug. ndi 9- Aug. Sanalandirebe mphoto zawo. FUSO KODI NANGA YABANDO ADZIVUTIKILASO NGATI SANAPEZE MPHOTO? Tikukufuna muyambe kuleka ngati momwe amandilira olosera bwino m'buyomu lachiwili lirilose. ZIKOMO.
Tipepese kuti vuto lotumiza mphoto zanu pa nthawi yake silinakonzedwebe koma tikuyesetsa kuti muzilandira Lachiwiri lililonse ngati kale. Pepani.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores