M'chitidwe ozikundikila ndalama komanso kupatsana maudindo motsatsatira ndondomeko kukupangitsa kuti mpira usapite patsogolo mdziko muno.
Khalakale pa ntchito ya uphunzitsi, Leo Mpulula, wanena izi.
Zoonadi Dyela Kmanso Kusowa Chilungamo Ndkomwedi Mpila Sukusuntha
Lufazili Anatisiyila Mavuto, Ma Banker's Tikulila
Mabanka sizikutiyenderadi pano.